Masalimo 20:3 - Buku Lopatulika3 likumbukire zopereka zako zonse, lilandire nsembe yako yopsereza; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 likumbukire zopereka zako zonse, lilandire nsembe yako yopsereza; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Alandire zopereka zako zonse, akondwere ndi nsembe zako zopsereza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Iye akumbukire nsembe zako zonse ndipo alandire nsembe zako zopsereza. Sela Onani mutuwo |