Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 20:2 - Buku Lopatulika

2 likutumizire thandizo lotuluka m'malo oyera, ndipo likugwirizize kuchokera mu Ziyoni;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 likutumizire thandizo lotuluka m'malo oyera, ndipo likugwirizize kuchokera m'Ziyoni;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Akutumizire chithandizo kuchokera ku malo ake oyera, akuchirikize kuchokera ku Ziyoni.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Iye atumize thandizo kuchokera ku malo ake opatulika; akugwirizize kuchokera ku Ziyoni.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 20:2
12 Mawu Ofanana  

Chinkana anatero Davide anathyola linga la Ziyoni, lomwelo ndilo mzinda wa Davide.


Ndipo pamene adalowa nalo likasa la Mulungu analiika pamalo pake pakati pa hema amene Davide adaliutsira; ndipo Davide anapereka nsembe zopsereza, ndi nsembe zoyamika pamaso pa Yehova.


Ndipo anadulitsa ndi matabwa amkungudza mikono makumi awiri m'kati mwa nyumba m'tsogolo mwake, kuyambira pansi kulekeza kumitanda; ichi anamanga kukhala chipinda chamkati, malo opatulika kwambiri.


Ndifuula kwa Yehova ndi mau anga, ndipo andiyankha m'phiri lake loyera.


Pakuti alendo andiukira, ndipo oopsa afunafuna moyo wanga; sadziikira Mulungu pamaso pao.


mpaka ndinalowa m'zoyera za Mulungu, ndi kulingalira chitsiriziro chao.


Dzina la Yehova ndilo nsanja yolimba; wolungama athamangiramo napulumuka.


Tafuula, takuwa iwe, wokhala mu Ziyoni, chifukwa Woyera wa Israele wa m'kati mwako ali wamkulu.


Ndipo adzayankhanji amithenga a amitundu? Kuti Yehova wakhazikitsa Ziyoni, ndipo m'menemo anthu ake ovutidwa adzaona pobisalira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa