Masalimo 19:11 - Buku Lopatulika11 Ndiponso kapolo wanu achenjezedwa nazo, m'kuzisunga izo muli mphotho yaikulu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndiponso kapolo wanu achenjezedwa nazo, m'kuzisunga izo muli mphotho yaikulu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Malamulo anu amandiwunikira ine mtumiki wanu, poŵasunga ndimalandira mphotho yaikulu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Mtumiki wanu amachenjezedwa nawo; powasunga pali mphotho yayikulu. Onani mutuwo |