Masalimo 19:10 - Buku Lopatulika10 Ndizo zifunika koposa golide, inde, golide wambiri woyengetsa; zizuna koposa uchi ndi zakukha za zisa zake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndizo zifunika koposa golide, inde, golide wambiri woyengetsa; zizuna koposa uchi ndi zakukha za zisa zake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Zonsezi nzoyenera kuzikhumbira kupambana golide, ngakhale golide wambiri wamtengowapatali, nzotsekemera kupambana uchi, ngakhale uchi wozuna kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 ndi a mtengowapatali kuposa golide, kuposa golide weniweni; ndi otsekemera kuposa uchi, kuposa uchi wochokera pa chisa chake. Onani mutuwo |