Masalimo 18:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo Iye anaweramitsa thambo, natsika; ndipo pansi pa mapazi ake panali mdima bii. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo Iye anaweramitsa thambo, natsika; ndipo pansi pa mapazi ake panali mdima bii. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Adang'amba thambo natsika pansi, mdima wabii unali ku mapazi ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Iye anangʼamba thambo natsika pansi; pansi pa mapazi ake panali mitambo yakuda. Onani mutuwo |