Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 18:10 - Buku Lopatulika

10 Ndipo anaberekeka pa kerubi, nauluka; nauluka msanga pa mapiko a mphepo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Ndipo anaberekeka pa kerubi, nauluka; nauluka msanga pa mapiko a mphepo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Adakwera pa mkerubi nauluka. Adayenda mwaliŵiro ndi mphepo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Iye anakwera pa Kerubi ndi kuwuluka; nawuluka ndi mphepo mwaliwiro.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 18:10
8 Mawu Ofanana  

Amene alumikiza mitanda ya zipinda zake m'madzi; naika makongwa akhale agaleta ake; nayenda pa mapiko a mphepo.


Weramutsani thambo lanu, Yehova, nimutsike: Khudzani mapiri ndipo adzafuka.


Mbusa wa Israele, tcherani khutu; inu wakutsogolera Yosefe ngati nkhosa; inu wokhala pa akerubi, walitsani.


Yehova ndiye mfumu; mitundu ya anthu injenjemere; Iye akhala pakati pa akerubi; dziko lapansi ligwedezeke.


Ife takhala ngati iwo amene simunawalamulire konse, ngati iwo amene sanatchedwe dzina lanu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa