Masalimo 18:11 - Buku Lopatulika11 Anaika mdima pobisala pake, hema wake womzinga; mdima wa madzi, makongwa a kuthambo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Anaika mdima pobisala pake, hema wake womzinga; mdima wa madzi, makongwa a kuthambo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Mdima adausandutsa chofunda chake, mitambo yakuda yamvula adaisandutsa mwafuli wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Iye anapanga mdima kukhala chofunda chake, chophimba chake chomuzungulira chinali mitambo yakuda ya mlengalenga. Onani mutuwo |