Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 18:12 - Buku Lopatulika

12 Mwa kuchezemira kunali pamaso pake makongwa anakanganuka, matalala ndi makala amoto.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Mwa kuchezemira kunali pamaso pake makongwa anakanganuka, matalala ndi makala amoto.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 M'kuŵala kumene kunali pamaso pake, munkafumira matalala ndi makala amoto, amene adabzola mitambo yophimba ija.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Mʼkuwala kumene kunali pamaso pake munkachokera matalala, makala amoto ndi ziphaliwali zongʼanima.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 18:12
11 Mawu Ofanana  

muvala ulemu ndi chifumu. Amene mudzikuta nako kuunika monga ndi chovala; ndi kuyala thambo ngati nsalu yotchinga.


Ndipo Yehova anati kwa Mose, Taona, ndikudza kwa iwe mu mtambo wakuda bii, kuti anthu amve pamene ndilankhula ndi iwe, ndi kuti akuvomereze nthawi zonse. Pakuti Mose adauza Yehova mau a anthuwo.


Ndiveka thambo ndi kuda, ndi kuyesa chiguduli chofunda chake.


ndipo Iye anasandulika pamaso pao; ndipo nkhope yake inawala monga dzuwa, ndi zovala zake zinakhala zoyera mbuu monga kuwala.


Akali chilankhulire, onani, mtambo wowala unawaphimba iwo: ndipo onani, mau ali kunena mumtambo, Uyu ndiye Mwana wanga wokondedwa, mwa iyeyu ndikondwera, mverani Iye.


Ndipo kunali, pakuthawa iwo pamaso pa Israele, potsikira pa Betehoroni, Yehova anawagwetsera miyala yaikulu yochokera kumwamba mpaka pa Azeka, nafa iwo; akufa ndi miyala yamatalala anachuluka ndi iwo amene ana a Israele anawapha ndi lupanga.


Ndipo anatsika kumwamba matalala aakulu, lonse lolemera ngati talente, nagwa pa anthu; ndipo anthu anachitira Mulungu mwano chifukwa cha mliri wa matalala, pakuti mliri wake ndi waukulu ndithu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa