Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 18:5 - Buku Lopatulika

5 Zingwe za manda zindizinga, misampha ya imfa inandifikira ine.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Zingwe za manda zindizinga, misampha ya imfa inandifikira ine.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Nthambo zakumanda zidandizeŵeza, misampha ya imfa idandikola.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Anandimanga ndi zingwe za ku manda; misampha ya imfa inalimbana nane.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 18:5
8 Mawu Ofanana  

Zingwe za imfa zinandizinga, ndi zowawa za manda zinandigwira: ndinapeza nsautso ndi chisoni.


Akadatimiza madziwo, mtsinje ukadapita pa moyo wathu;


Mundiyankhe Yehova; pakuti chifundo chanu nchokoma; munditembenukire monga mwa unyinji wa nsoni zokoma zanu.


Pakuti chifundo chanu cha pa ine nchachikulu; ndipo munalanditsa moyo wanga kunsi kwa manda.


Pakuti munthu sadziwatu mphindi yake; monga nsomba zigwidwa mu ukonde woipa, ndi mbalame zikodwa mumsampha, momwemo ana a anthu amagwidwa ndi nthawi ya tsoka, ngati msampha umene uwagwera modzidzimuka.


yemweyo Mulungu anamuukitsa, atamasula zowawa za imfa, mwakuti sikunali kotheka kuti Iye agwidwe nayo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa