Masalimo 18:4 - Buku Lopatulika4 Zingwe za imfa zinandizinga, ndipo mitsinje ya zopanda pake inandiopsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Zingwe za imfa zinandizinga, ndipo mitsinje ya zopanda pake inandiopsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Nthambo za imfa zidandizungulira, mitsinje yothamanga yoononga idandisefukira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Zingwe za imfa zinandizinga; mitsinje yothamanga yachiwonongeko inandiopsa kwambiri. Onani mutuwo |