Masalimo 18:3 - Buku Lopatulika3 Ndidzaitanira Yehova, woyenera kutamandika, ndipo adzandipulumutsa ine kwa adani anga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndidzaitanira Yehova, woyenera kutamandika, ndipo adzandipulumutsa ine kwa adani anga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ndimaitana Chauta, amene ayenera kumtamanda, ndipo amandipulumutsa kwa adani anga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ndimayitana Yehova amene ndi woyenera matamando, ndipo ndapulumutsidwa kwa adani anga. Onani mutuwo |