Masalimo 18:44 - Buku Lopatulika44 Pakumva m'khutu za ine adzandimvera, alendo adzandigonjera monyenga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 Pakumva m'khutu za ine adzandimvera, alendo adzandigonjera monyenga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 Atangomva za ine adayamba kundimvera, anthu a maiko ena adabwera kwa ine kudzapemba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 Alendo amadzipereka okha pamaso panga; akangomva za ine amandigonjera. Onani mutuwo |