Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 18:40 - Buku Lopatulika

40 Ndipo adani anga mwawalozetsa m'mbuyo kwa ine, kuti ndipasule ondidawo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

40 Ndipo adani anga mwawalozetsa m'mbuyo kwa ine, kuti ndipasule ondidawo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

40 Inu mudapirikitsa adani anga kuti andithaŵe, amene ankadana nane ndidaŵaononga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

40 Inu munachititsa adani anga kutembenuka, kuonetsa misana yawo pothawa, ndipo ine ndinawononga adani angawo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 18:40
3 Mawu Ofanana  

Mwezi wakhumi ndi chiwiri tsono, ndiwo mwezi wa Adara, tsiku lake lakhumi ndi chitatu, mau a mfumu ndi lamulo lake ali pafupi kuchitika, tsikuli adani a Ayuda anayesa kuwachitira ufumu, koma chinasinthika; popeza Ayuda anachitira ufumu iwo odana nao;


Pakuti mudzawabweza m'mbuyo, popiringidza m'nsinga zanu pankhope pao.


Ndipo anawabwezera zopanda pake zao, nadzawaononga m'choipa chao; Yehova Mulungu wathu adzawaononga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa