Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 18:32 - Buku Lopatulika

32 Mulungu ndiye wondizingiza mphamvu m'chuuno, nakonza njira yanga ikhale yangwiro.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

32 Mulungu ndiye wondizingiza mphamvu m'chuuno, nakonza njira yanga ikhale yangwiro.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

32 Mulungu wathu ndiye amene amandiveka mphamvu, wandichotsera zoopsa m'njira zanga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

32 Ndi Mulungu amene anandipatsa mphamvu ndi kulungamitsa njira yanga.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 18:32
8 Mawu Ofanana  

Mulungu ndiye linga langa lamphamvu; ndipo Iye ayendetsa angwiro mu njira yake.


Yehova ndiye mphamvu yanga, ndi chikopa changa; mtima wanga wakhulupirira Iye, ndipo anandithandiza, chifukwa chake mtima wanga ukondwera kwakukulu; ndipo ndidzamyamika nayo nyimbo yanga.


Ndidzati kwa Yehova, Pothawirapo panga ndi linga langa; Mulungu wanga, amene ndimkhulupirira.


Yehova achita ufumu; wadziveka ndi ukulu; wadziveka Yehova, wadzimangirira mphamvu m'chuuno; dziko lomwe lokhalamo anthu likhakizika, silidzagwedezeka.


Musaope inu, musakhale ndi mantha; kodi ndinanena kwa iwe zakale, ndi kuzionetsa zimenezo, ndipo inu ndinu mboni zanga. Kodi popanda Ine aliponso Mulungu? Iai, palibe thanthwe; sindidziwa lililonse.


Ine ndili Yehova, ndipo palibe winanso; popanda Ine palibe Mulungu; ndidzakumanga m'chuuno, ngakhale sunandidziwe;


si kuti tili okwanira pa ife tokha, kuyesera kanthu monga mochokera mwa ife tokha; kukwanira kwathu kuchokera kwa Mulungu;


Ndipo kunalinso nkhondo; ndipo Davide anatuluka, nakamenyana ndi Afilisti, nawapha ndi maphedwe aakulu, ndipo iwo anamthawa iye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa