Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 18:33 - Buku Lopatulika

33 Alinganiza mapazi anga ngati a mbawala, nandiimitsa pamsanje panga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

33 Alinganiza mapazi anga ngati a mbawala, nandiimitsa pamsanje panga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

33 Amalimbitsa miyendo yanga ngati ya mbaŵala, ndipo amandisunga bwino m'mapiri.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

33 Iye amasandutsa mapazi anga kukhala ngati ambawala yayikazi; Iye amandithandiza kuyimirira pamwamba pa mapiri.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 18:33
6 Mawu Ofanana  

Ndipo analipo ana atatu a Zeruya, ndiwo Yowabu, Abisai ndi Asahele. Ndipo Asahele anali waliwiro ngati mbawala.


Yehova anagunda kumwamba; ndipo Wam'mwambamwamba ananena mau ake.


Ine ndili Yehova, ndipo palibe winanso; popanda Ine palibe Mulungu; ndidzakumanga m'chuuno, ngakhale sunandidziwe;


Yehova, Ambuye, ndiye mphamvu yanga, asanduliza mapazi anga ngati a mbawala, nadzandipondetsa pa misanje yanga.


Anamuyendetsa pa misanje ya dziko lapansi, ndipo anadya zipatso za m'minda; namyamwitsa uchi wa m'thanthwe, ndi mafuta m'mwala wansangalabwe;


Wodala iwe, Israele; akunga iwe ndani, mtundu wa anthu opulumutsidwa ndi Yehova, ndiye chikopa cha thandizo lako, Iye amene akhala lupanga la ukulu wako! Ndi adani ako adzakugonjera; ndipo udzaponda pa misanje yao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa