Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 18:25 - Buku Lopatulika

25 Pa wachifundo mukhala wachifundo; pa munthu wangwiro mukhala wangwiro.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Pa wachifundo mukhala wachifundo; pa munthu wangwiro mukhala wangwiro.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Kwa anthu okhulupirika, Inu Mulungu mumadziwonetsa okhulupirika. Kwa anthu aungwiro, mumadziwonetsa abwino kotheratu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Kwa wokhulupirika, Inu mumaonetsa kukhulupirika kwanu; kwa anthu amakhalidwe abwino, Inu mumaonetsanso makhalidwe abwino,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 18:25
14 Mawu Ofanana  

mverani Inu pamenepo m'mwambamo, ndipo chitani, weruzani akapolo anu, kumtsutsa woipayo, ndi kumbwezera tchimo lake, ndi kulungamitsa wolungamayo kumbwezera monga chilungamo chake.


nakana kumvera, osakumbukiranso zodabwitsa zanu munazichita pakati pao; koma anaumitsa khosi lao, ndipo m'kupanduka kwao anaika mtsogoleri abwerere kunka ku ukapolo wao; koma Inu ndinu Mulungu wokhululukira, wachisomo, ndi wansoni, wolekereza, ndi wochuluka chifundo; ndipo simunawasiye.


ukakhala woyera ndi woongoka mtima, zoonadi adzakugalamukira tsopano, ndi kupindulitsa pokhala pako polungama.


Chifundonso ndi chanu, Ambuye, Chifukwa Inu mubwezera munthu aliyense monga mwa ntchito yake.


Njira ya wolungama ili njira yoongoka; Inu amene muli woongoka, mukonza njira ya wolungama.


Odala ali akuchitira chifundo; chifukwa adzalandira chifundo.


Ndipo tsono tidzatani? Kodi chilipo chosalungama ndi Mulungu? Msatero ai.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa