Masalimo 18:24 - Buku Lopatulika24 Ndimo anandisudzulira Yehova monga mwa chilungamo changa, monga mwa kusisira kwa manja anga pamaso pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndimo anandisudzulira Yehova monga mwa chilungamo changa, monga mwa kusisira kwa manja anga pamaso pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Nchifukwa chake Chauta wandipatsa mphotho molingana ndi ntchito zanga zabwino, monga momwe akuwonera kuti ndilibe mlandu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Yehova wandipatsa mphotho molingana ndi chilungamo changa, molingana ndi kuyera kwa manja anga pamaso pake. Onani mutuwo |