Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 18:26 - Buku Lopatulika

26 Pa woyera mtima mukhala woyera mtima; pa wotsutsatsutsa mukhala wotsutsana naye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 Pa woyera mtima mukhala woyera mtima; pa wotsutsatsutsa mukhala wotsutsana naye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

26 Kwa anthu oyera mtima mumadziwonetsa okoma mtima, koma kwa anthu oipa mtima, mumawonetsa kunyansidwa nawo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 kwa woyera mtima, Inu mumaonetsa kuyera mtima kwanu, koma kwa achinyengo mumaonetsanso kunyansidwa nawo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 18:26
9 Mawu Ofanana  

Anyozadi akunyoza, koma apatsa akufatsa chisomo.


Kodi adzati, Nyumba ya Yakobo iwe, Mzimu wa Yehova waperewera kodi? Izi ndi ntchito zake kodi? Mau anga samchitira zokoma kodi, iye amene ayenda choongoka?


nsautso ndi kuwawa mtima, kwa moyo wa munthu aliyense wakuchita zoipa, kuyambira Myuda, komanso Mgriki;


Pakuti chiweruziro chilibe chifundo kwa iye amene sanachite chifundo; chifundo chidzitamandira kutsutsana nacho chiweruziro.


Chifukwa chake Yehova Mulungu wa Israele akuti, Ndinaterodi kuti banja lako ndi banja la kholo lako lidzayenda pamaso panga nthawi zonse; koma tsopano Yehova ati, Chikhale kutali ndi Ine; popeza amene andilemekeza Ine, Inenso ndidzawalemekeza iwowa, ndipo akundipeputsa Ine, adzapeputsidwa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa