Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 18:22 - Buku Lopatulika

22 Pakuti maweruzo ake onse anali pamaso panga, ndipo malemba ake sindinawachotse kwa ine.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Pakuti maweruzo ake onse anali pamaso panga, ndipo malemba ake sindinawachotsa kwa ine.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Ndidamvera malangizo ake onse, ndipo malamulo ake sindidaŵataye.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Malamulo ake onse ali pamaso panga; sindinasiye malangizo ake.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 18:22
9 Mawu Ofanana  

Phazi langa lagwiratu moponda Iye, ndasunga njira yake, wosapatukamo.


Ndinalingitsa mtima wanga uchite malemba anu, kosatha, kufikira chimaliziro.


Mundigwirizize ndipo ndidzapulumutsidwa, ndipo ndidzasamalira malemba anu chisamalire.


Chifukwa chake ndiyesa ngolunjika malangizo anu onse akunena zonse; koma ndidana nazo njira zonse zonyenga.


Ndinafotokozera ndi milomo yanga maweruzo onse a pakamwa panu.


Ndinasankha njira yokhulupirika; ndinaika maweruzo anu pamaso panga.


Zitapita izi Yesu anampeza mu Kachisi, nati kwa iye, Taona, wachiritsidwa; usachimwenso, kuti chingakugwere choipa choposa.


Ndipo munene pamaso pa Yehova Mulungu wanu, Ndachotsa zopatulika m'nyumba mwanga, ndi kuzipereka kwa Mlevi, ndi kwa mlendo, ndi kwa mwana wamasiye, ndi kwa mkazi wamasiye, monga mwa lamulo lanu lonse munandilamulira ine; sindinalakwire malamulo anu, kapena kuwaiwala.


Sindinadyeko m'chisoni changa, kapena kuchotsako podetsedwa, kapena kuperekako kwa akufa; ndamvera mau a Yehova Mulungu wanga; ndachita monga mwa zonse munandilamulira ine.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa