Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 18:23 - Buku Lopatulika

23 Ndipo ndinakhala wangwiro ndi Iye, ndipo ndinadzisunga wosachita choipa changa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Ndipo ndinakhala wangwiro ndi Iye, ndipo ndinadzisunga wosachita choipa changa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Ndinalibe mlandu pamaso pake, ndinkalewa zoipa m'moyo mwanga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Ndakhala moyo wosalakwa pamaso pake ndipo ndakhala ndi kupewa tchimo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 18:23
9 Mawu Ofanana  

Ndidziwanso, Mulungu wanga, kuti muyesa mtima, nimukondwera nako kuongoka. Koma ine, ndi mtima wanga woongoka ndapereka zonsezi mwaufulu; ndipo tsopano ndaona mokondwera anthu anu okhala pompano, napereka kwa Inu mwaufulu.


Pakuti Yehova ndiye wolungama; akonda zolungama; woongoka mtima adzapenya nkhope yake.


Ndinasankha njira yokhulupirika; ndinaika maweruzo anu pamaso panga.


Mwayesera mtima wanga; mwandizonda usiku; mwandisuntha, simupeza kanthu; mwatsimikiza mtima kuti m'kamwa mwanga simudzalakwa.


Siyana nacho choipa, nuchite chokoma, nukhale nthawi zonse.


Ndipo Yehova adzabwezera munthu yense chilungamo chake ndi chikhulupiriko chake, popeza Yehova anakuperekani lero m'dzanja langa, koma sindinalole kutukulira dzanja langa pa wodzozedwa wa Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa