Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 18:19 - Buku Lopatulika

19 Ananditulutsanso andifikitse motakasuka; anandilanditsa, pakuti anakondwera ndi ine.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 Ananditulutsanso andifikitse motakasuka; anandilanditsa, pakuti anakondwera ndi ine.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 Adakandifikitsa ku malo amtendere, adandipulumutsa chifukwa adakondwera nane.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 Iye anandipititsa kumalo otakasuka; anandipulumutsa chifukwa amakondwera nane.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 18:19
8 Mawu Ofanana  

Wolemekezeka Yehova Mulungu wanu amene anakondwera nanu, kukuikani pa mpando wachifumu wa Israele; popeza Yehova anakonda Israele nthawi yosatha, chifukwa chake anakulongani inu ufumu, kuti muchite chiweruzo ndi chilungamo.


Inde akadakukopani muchoke posaukira, mulowe kuchitando kopanda chopsinja; ndipo zoikidwa pagome panu zikadakhala zonona ndithu.


M'mene ndinasautsika ndinaitanira pa Yehova; anandiyankha nandiika motakasuka Yehova.


Mwandipondetsa patalipatali, sanaterereke mapazi anga.


Ndipo simunandipereke m'dzanja la mdani; munapondetsa mapazi anga pali malo.


Yehova akhazikitsa mayendedwe a munthu; ndipo akondwera nayo njira yake.


Ndipo anandikweza kunditulutsa m'dzenje la chitayiko, ndi m'thope la pachithaphwi; nandipondetsa pathanthwe, nakhazika mayendedwe anga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa