Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 18:16 - Buku Lopatulika

16 Anatuma kuchokera m'mwamba, ananditenga; anandivuula m'madzi ambiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Anatuma kuchokera m'mwamba, ananditenga; anandivuula m'madzi ambiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Ali kumwamba Chauta adatambalitsa dzanja nandigwira, ndi kundivuula m'madzi ozama.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Ali kumwamba, Iye anatambalitsa dzanja lake ndipo anandigwira; anandivuwula mʼmadzi ozama.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 18:16
10 Mawu Ofanana  

Iye anatumiza kuchokera kumwamba nanditenga; Iye ananditulutsa m'madzi aakulu.


Tulutsani manja anu kuchokera m'mwamba; ndikwatuleni ndi kundilanditsa kumadzi aakulu, kudzanja la alendo;


Mwandipulumutsa pa zolimbana nane za anthu; mwandiika mutu wa amitundu; mtundu wa anthu sindinaudziwe udzanditumikira.


Chifukwa chake oyera mtima onse apemphere kwa Inu, pa nthawi ya kupeza Inu; indetu pakusefuka madzi aakulu sadzamfikira iye.


Adzanditumizira m'mwamba, nadzandipulumutsa ponditonza wofuna kundimeza; Mulungu adzatumiza chifundo chake ndi choonadi chake.


Ndipo atakula mwanayo, anapita naye kwa mwana wamkazi wa Farao, ndipo iye anakhala mwana wake. Ndipo anamutcha dzina lake Mose, nati, Chifukwa ndinamvuula m'madzi.


Adzudzula nyanja, naiphwetsa, naumitsa mitsinje yonse; Basani ndi Karimele afota, ndi duwa la ku Lebanoni linyala.


Ndipo anena ndi ine, Madziwo udawaona uko akhalako mkazi wachigololoyo ndiwo anthu, ndi makamu, ndi mitundu, ndi manenedwe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa