Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 17:9 - Buku Lopatulika

9 kundilanditsa kwa oipa amene andipasula, adani a pa moyo wanga amene andizinga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 kundilanditsa kwa oipa amene andipasula, adani a pa moyo wanga amene andizinga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 kuti asandiwone anthu oipa ofuna kupasula, ndiye kuti adani anga oopsaŵa amene akundizinga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 kuchoka kwa oyipa amene amandizinga ine, kuchoka kwa anthu amene ndi adani anga, amene andizungulira ine.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 17:9
8 Mawu Ofanana  

Ndipo ndaikira anthu anga Israele malo, ndi kuwaoka, kuti akhale m'malo mwao osasunthikanso; ndi ana osalungama sadzawapululanso monga poyamba paja;


Pobisalira pamaso panu mudzawabisa kwa chiwembu cha munthu, mudzawabisa iwo mumsasa kuti muwalanditse pa kutetana kwa malilime.


Andibwezera choipa m'malo mwa chokoma, inde, asaukitsa moyo wanga.


Athe nzeru nachite manyazi iwo akufuna moyo wanga; abwezedwe m'mbuyo nasokonezeke iwo akundipangira chiwembu.


Pakuti ananditchera ukonde wao m'mbunamo kopanda chifukwa, anakumbira moyo wanga dzenje kopanda chifukwa.


mdani alondole moyo wanga, naupeze; naupondereze pansi moyo wanga, naukhalitse ulemu wanga m'fumbi.


Ndipo Saulo anamuka mbali ina ya phiri, Davide ndi anthu ake kuseri kwake; ndipo Davide anafulumira kuthawa, chifukwa cha kuopa Saulo; popeza Saulo ndi anthu ake anazinga Davide ndi anthu ake kwete kuti awagwire.


Ndiponso atate wanga, penyani, inde penyani mkawo wa mwinjiro wanu m'dzanja langa; popeza ndinadula mkawo wa mwinjiro wanu, osakuphani, mudziwe, nimuone kuti mulibe choipa kapena kulakwa m'dzanja langa, ndipo sindinakuchimwirani, chinkana inu musaka moyo wanga kuti muugwire.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa