Masalimo 17:10 - Buku Lopatulika10 Mafuta ao awatsekereza; m'kamwa mwao alankhula modzikuza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Mafuta ao awatsekereza; m'kamwa mwao alankhula modzikuza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Mitima yao ilibe chifundo, amalankhula modzikuza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Iwo amatseka mitima yawo yopanda chifundo, ndi pakamwa pawo amayankhula modzitamandira. Onani mutuwo |