Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 17:11 - Buku Lopatulika

11 Tsopano anatizinga m'mayendedwe athu, apenyetsetsa m'maso kuti atigwetse pansi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Tsopano anatizinga m'mayendedwe athu, apenyetsetsa m'maso kuti atigwetse pansi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Amangondilondola ndi kundizinga. Amandiyang'ana kuti apeze njira yondigwetsera pansi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Andisaka, tsopano andizungulira ndi maso awo atcheru, kuti andigwetse pansi.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 17:11
7 Mawu Ofanana  

Oipa anasolola lupanga, nakoka uta wao; alikhe ozunzika ndi aumphawi, aphe amene ali oongoka m'njira.


Zinandizungulira ngati madzi tsiku lonse; zinandizinga pamodzi.


Ndipo Saulo anamuka mbali ina ya phiri, Davide ndi anthu ake kuseri kwake; ndipo Davide anafulumira kuthawa, chifukwa cha kuopa Saulo; popeza Saulo ndi anthu ake anazinga Davide ndi anthu ake kwete kuti awagwire.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa