Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 17:12 - Buku Lopatulika

12 Afanana ndi mkango wofuna kumwetula, ndi msona wa mkango wakukhala mobisalamo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Afanana ndi mkango wofuna kumwetula, ndi msona wa mkango wakukhala mobisalamo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Ali ngati mkango wofunitsitsa kuti ukadzule, ngati chilombo cholusa cholalira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Iwo ali ngati mkango wofuna nyama; ngati mkango waukulu wokhala mobisala.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 17:12
5 Mawu Ofanana  

Alalira monga mkango m'ngaka mwake; alalira kugwira wozunzika, agwira wozunzika, pakumkola mu ukonde mwake.


Andiyasamira m'kamwa mwao, ngati mkango wozomola ndi wobangula.


kuti angamwetule moyo wanga ngati mkango, ndi kuukadzula, wopanda wina wondilanditsa.


Koma Ambuye anaima nane nandipatsa mphamvu; kuti mwa ine chilalikiro chimveke konsekonse, ndi amitundu onse amve; ndipo ndinalanditsidwa m'kamwa mwa mkango.


Khalani odzisungira, dikirani; mdani wanu mdierekezi, monga mkango wobuma, ayendayenda ndi kufunafuna wina akamlikwire:


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa