Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 17:5 - Buku Lopatulika

5 M'mayendedwe anga ndasunga mabande anu, mapazi anga sanaterereke.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 M'mayendedwe anga ndasunga mabande anu, mapazi anga sanaterereke.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Ndayenda m'njira zanu nthaŵi zonse, sindidapatuke konse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Mayendedwe anga akhazikika pa njira zanu; mapazi anga sanaterereke.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 17:5
12 Mawu Ofanana  

Phazi langa lagwiratu moponda Iye, ndasunga njira yake, wosapatukamo.


Khazikitsani mapazi anga m'mau anu; ndipo zisandigonjetse zopanda pake zilizonse.


Sadzalola phazi lako literereke: Iye amene akusunga sadzaodzera.


Yehova adzakusunga kukuchotsera zoipa zilizonse; adzasunga moyo wako.


Mwandipondetsa patalipatali, sanaterereke mapazi anga.


Ndidzalondola adani anga, ndi kuwapeza, ndipo sindidzabwerera asanathe psiti.


Pakuti ndinati, Asakondwerere ine; pakuterereka phazi langa, asadzikuze pa ine.


Mtima wathu sunabwerere m'mbuyo, ndipo m'mayendedwe athu sitinapatuke m'njira yanu;


Pamene ndinati, Literereka phazi langa, chifundo chanu, Yehova, chinandichirikiza.


Inu Yehova, ndidziwa kuti njira ya munthu sili mwa iye mwini; sikuli kwa munthu woyenda kulongosola mapazi ake.


Adzasunga mapazi a okondedwa ake, koma oipawo adzawakhalitsa chete mumdima; pakuti palibe munthu adzapambana ndi mphamvu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa