Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 17:6 - Buku Lopatulika

6 Ine ndinakuitanani, pakuti mudzandiyankha, Mulungu; tcherani khutu lanu kwa ine, imvani mau anga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Ine ndinakuitanani, pakuti mudzandiyankha, Mulungu; tcherani khutu lanu kwa ine, imvani mau anga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Ndikupemphera kwa Inu Mulungu, chifukwa mudzandiyankha. Tcherani khutu kuti mumve mau anga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Ine ndikuyitana Inu, Mulungu wanga, pakuti mudzandiyankha; tcherani khutu lanu kwa ine ndipo mumve pemphero langa.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 17:6
10 Mawu Ofanana  

Popeza amanditcherera khutu lake, chifukwa chake ndidzaitanira Iye masiku anga onse.


Chitani chinthenthe, ndipo musachimwe. Nenani mumtima mwanu pakama panu, ndipo mukhale chete.


Koma ine ndidzafuulira kwa Mulungu; ndipo Yehova adzandipulumutsa.


Tsiku la msauko wanga ndidzaitana Inu; popeza mudzandivomereza.


Pemphero langa lidze pamaso panu; munditcherere khutu kukuwa kwanga.


Tcherani makutu anu, Yehova, nimumve; tsegulani maso anu, Yehova, nimuone; ndi kumva mau onse a Senakeribu, amene watumiza kumtonza Mulungu wamoyo.


Chifukwa chake, Yehova, Mulungu wathu, mutipulumutse ife m'manja mwake, kuti maufumu onse a dziko adziwe, kuti Inu ndinu Yehova, Inu nokha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa