Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 17:2 - Buku Lopatulika

2 Pankhope panu patuluke chiweruzo changa; maso anu apenyerere zolunjika.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Pankhope panu patuluke chiweruzo changa; maso anu apenyerere zolunjika.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Kusalakwa kwanga kuwonekere poyera pa chiweruzo chanu, maso anu aone kulungama kwanga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Kusalakwa kwanga kuchokera kwa inu; maso anu aone chimene ndi cholungama.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 17:2
8 Mawu Ofanana  

Yehova sadzamsiya m'dzanja lake; ndipo sadzamtsutsa poweruzidwa iye.


Ndipo adzaonetsa chilungamo chako monga kuunika, ndi kuweruza kwako monga usana.


Koma mukuti, Njira ya Ambuye njosayenera. Tamvera tsono nyumba ya Israele, Kodi njira yanga njosayenera? Njira zanu si ndizo zosayenera?


Koma nyumba ya Israele imanena, Njira ya Ambuye njosayenera. Inu, nyumba ya Israele, kodi njira zanga nzosayenera? Njira zanu si ndizo zosayenera?


Koma ana a anthu a mtundu wako akuti, Njira ya Ambuye siiyenera; koma iwowa njira yao siiyenera.


Koma munati, Njira ya Ambuye siiyenera. Nyumba ya Israele inu, ndidzakuweruzani, yense monga mwa njira zake.


Ndipo kwa Iye amene akhoza kukudikirani mungakhumudwe, ndi kukuimikani pamaso pa ulemerero wake opanda chilema m'kukondwera,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa