Masalimo 15:3 - Buku Lopatulika3 Amene sasinjirira ndi lilime lake, nachitira mnzake choipa, ndipo satola miseche pa mnansi wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Amene sasinjirira ndi lilime lake, nachitira mnzake choipa, ndipo satola miseche pa mnansi wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ndi amene sasinjirira ndipo sachita anzake zoipa, kapena kumafalitsa mbiri yoipa ya anzake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 ndipo mʼkamwa mwake simutuluka mawu osinjirira, amene sachitira choyipa mnansi wake kapena kufalitsa mbiri yoyipa ya munthu mnzake, Onani mutuwo |