Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 149:5 - Buku Lopatulika

5 Okondedwa ake atumphe mokondwera mu ulemu: Afuule mokondwera pamakama pao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Okondedwa ake atumphe mokondwera m'ulemu: Afuule mokondwera pamakama pao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Okhulupirika akondwerere chigonjetso chopambanachi, aziimba mokondwa ali gone pa mabedi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Oyera mtima asangalale mu ulemu wake ndi kuyimba mwachimwemwe pa mabedi awo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 149:5
12 Mawu Ofanana  

Chomwecho Davide ndi a nyumba yonse ya Israele anakwera nalo likasa la Yehova, ndi chimwemwe ndi kulira kwa malipenga.


Koma palibe anganene, Ali kuti Mulungu Mlengi wanga, wakupatsa nyimbo usiku;


M'mahema a olungama muli liu lakufuula mokondwera Dzanja lamanja la Yehova ndi la chipulumutso:


Ndipo ansembe ake ndidzawaveka ndi chipulumutso: Ndi okondedwa ake adzafuulitsa mokondwera.


Ntchito zanu zonse zidzakuyamikani, Yehova; ndi okondedwa anu adzakulemekezani.


Yehova ndiye mbusa wanga; sindidzasowa.


Koma usana Yehova adzalamulira chifundo chake, ndipo usiku nyimbo yake idzakhala ndi ine. Inde pemphero la kwa Mulungu wa moyo wanga.


Kuonetsera chifundo chanu mamawa, ndi chikhulupiriko chanu usiku uliwonse.


ndi mlandu unakomera opatulika a Wam'mwambamwamba, nifika nthawi yakuti ufumu unali wao wa opatulikawo.


amene ife tikhoza kulowa naye ndi chikhulupiriro m'chisomo ichi m'mene tilikuimamo; ndipo tikondwera m'chiyembekezo cha ulemerero wa Mulungu.


amene mungakhale simunamuone mumkonda; amene mungakhale simumpenya tsopano, pokhulupirira, mukondwera naye ndi chimwemwe chosaneneka, ndi cha ulemerero:


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa