Masalimo 149:3 - Buku Lopatulika3 Alemekeze dzina lake ndi kuthira mang'ombe; amuimbire zomlemekeza ndi lingaka ndi zeze. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Alemekeze dzina lake ndi kuthira mang'ombe; amuimbire zomlemekeza ndi lingaka ndi zeze. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Atamande dzina lake povina, amuimbire nyimbo yokoma ndi ng'oma ndi pangwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Atamande dzina lake povina ndi kuyimbira Iye nyimbo ndi tambolini ndi pangwe. Onani mutuwo |