Masalimo 145:3 - Buku Lopatulika3 Yehova ndi wamkulu, nayenera kulemekezedwa kwakukulu; ndi ukulu wake ngwosasanthulika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Yehova ndi wamkulu, nayenera kulemekezedwa kwakukulu; ndi ukulu wake ngwosasanthulika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Chauta ndi wamkulu ndi woyenera kumtamanda kwambiri, ndipo ukulu wake sitingathe kuumvetsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Yehova ndi wamkulu ndi woyenera matamando onse; ukulu wake palibe angawumvetsetse. Onani mutuwo |