Masalimo 140:11 - Buku Lopatulika11 Munthu wamlomo sadzakhazikika padziko lapansi; choipa chidzamsaka munthu wachiwawa kuti chimgwetse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Munthu wamlomo sadzakhazikika pa dziko lapansi; choipa chidzamsaka munthu wachiwawa kuti chimgwetse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Musalole kuti woononga mbiri ya mnzake akhazikike m'dziko. Choipa chimlondole munthu wankhanza mpaka kumuwononga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Musalole kuti anthu achipongwe akhazikike mʼdziko; choyipa chilondole anthu ankhanza. Onani mutuwo |