Masalimo 14:1 - Buku Lopatulika1 Wauchitsiru amati mumtima mwake, Kulibe Mulungu. Achita zovunda, achita ntchito zonyansa; kulibe wakuchita bwino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Wauchitsiru amati mumtima mwake, Kulibe Mulungu. Achita zovunda, achita ntchito zonyansa; kulibe wakuchita bwino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Mumtima mwake munthu wopusa amati, “Kulibe Mulungu.” Anthu otereŵa ndi oipa, amachita zonyansa, palibe ndi mmodzi yemwe wochita zabwino. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Chitsiru chimati mu mtima mwake, “Kulibe Mulungu.” Oterewa ndi oyipa ndipo ntchito zawo ndi zonyansa; palibe amene amachita zabwino. Onani mutuwo |