Masalimo 139:9 - Buku Lopatulika9 Ndikadzitengera mapiko a mbandakucha, ndi kukhala ku malekezero a nyanja; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndikadzitengera mapiko a mbandakucha, ndi kukhala ku malekezero a nyanja; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ndikaulukira kotulukira dzuŵa, kapena kukafika kuzambwe, ku mathero a nyanja, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ngati ndiwulukira kotulukira dzuwa, ngati ndikakhala ku malekezero a nyanja, Onani mutuwo |