Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 139:10 - Buku Lopatulika

10 kungakhale komweko dzanja lanu lidzanditsogolera, nilidzandigwira dzanja lanu lamanja.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 kungakhale komweko dzanja lanu lidzanditsogolera, nilidzandigwira dzanja lanu lamanja.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 ngakhale kumenekonso mudzanditsogolera, dzanja lanu lamanja lidzandichirikiza.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 kumenekonso dzanja lanu lidzanditsogolera, dzanja lanu lamanja lidzandigwiriziza.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 139:10
6 Mawu Ofanana  

Atsitsimutsa moyo wanga; anditsogolera m'mabande a chilungamo, chifukwa cha dzina lake.


Moyo wanga uumirira Inu. Dzanja lamanja lanu lindigwiriziza.


Koma ndikhala ndi Inu chikhalire, mwandigwira dzanja langa la manja.


Pakuti Ine Yehova Mulungu wako ndidzagwira dzanja lako lamanja, ndi kunena kwa iwe, Usaope ndidzakuthandiza iwe.


Angakhale abisala pamwamba pa Karimele, ndidzawapwaira ndi kuwatenga komweko; angakhale abisala pamaso panga pansi pa nyanja, kumeneko ndidzalamulira njoka, ndipo idzawaluma.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa