Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 139:11 - Buku Lopatulika

11 Ndipo ndikati, Koma mdima undiphimbe, ndi kuunika kondizinga kukhale usiku.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndipo ndikati, Koma mdima undiphimbe, ndi kuunika kondizinga kukhale usiku.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Ndikanena kuti, “Mdima undiphimbe, kuŵala kumene kwandizinga kusanduke mdima,”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Ndikanena kuti, “Zoonadi, mdima udzandibisa ndithu ndipo kuwunika kukhale mdima mondizungulira,”

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 139:11
8 Mawu Ofanana  

Ndipo iye anauka pakati pa usiku, natenga mwana wanga kumimba kwanga, mdzakazi wanu ndili m'tulo, namuika m'mfukato mwake, naika mwana wake wakufa m'mfukato mwanga.


Avumbulutsa zozama mumdima, natulutsa mthunzi wa imfa ukhale poyera;


Palibe mdima kapena mthunzi wa imfa, kuti ochita zopanda pake abisaleko.


Ndipo amati, Yehova sachipenya, ndi Mulungu wa Yakobo sachisamalira.


Tsoka kwa iwo amene afunitsa kubisira Yehova uphungu wao, ndi ntchito zao zili mumdima, ndipo amati ndani ationa ife? Ndani atidziwa ife?


Kodi munthu angathe kubisala mobisika kuti ndisamuone iye? Ati Yehova. Kodi Ine sindidzala kumwamba ndi dziko lapansi? Ati Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa