Masalimo 139:12 - Buku Lopatulika12 Ungakhale mdima sudetsa pamaso panu, koma usiku uwala ngati usana; mdima ukunga kuunika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ungakhale mdima sudetsa pamaso panu, koma usiku uwala ngati usana; mdima ukunga kuunika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 ngakhale mdimawo, kwa Inu si mdima konse, kwa Inu usiku umaŵala ngati usana, mdima uli ngati kuŵala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 komabe mdimawo sudzakhala mdima kwa Inu; usiku udzawala ngati masana, pakuti mdima uli ngati kuwunika kwa Inu. Onani mutuwo |