Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 139:13 - Buku Lopatulika

13 Pakuti Inu munalenga impso zanga; munandiumba ndisanabadwe ine.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Pakuti Inu munalenga impso zanga; munandiumba ndisanabadwe ine.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Paja ndinu mudapanga za m'kati mwanga, mudandiwumba m'mimba mwa amai anga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Pakuti Inu munalenga za mʼkati mwanga; munandiwumba pamodzi mʼmimba mwa amayi anga.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 139:13
10 Mawu Ofanana  

Kodi Iye amene anandilenga ine m'mimba sanamlenge iyenso? Sindiye mmodzi anatiumba m'mimba?


Manja anu anandilenga nandiumba; mundizindikiritse, kuti ndiphunzire malemba anu.


Inu munandigwiriziza kuyambira ndisanabadwe, kuyambira pa thupi la mai wanga wondichitira zokoma ndinu; ndidzakulemekezani kosalekeza.


Tiyeni, tipembedze tiwerame; tigwade pamaso pa Yehova, amene anatilenga.


atero Yehova, amene anakutenga iwe, nakuumba kuchokera m'mimba, amene adzathangata iwe. Usaope Yakobo, mtumiki wanga ndi iwe, Yesuruni, amene ndakusankha iwe.


Mverani Ine, banja la Yakobo, ndi otsala onse a banja la Israele, amene ndakunyamulani kuyambira m'mimba, ndi kukusenzani chibadwire;


Ndisanakulenge iwe m'mimba ndinakudziwa, ndipo usanabadwe ndinakupatula iwe; ndinakuika kuti ukhale mneneri wa mitundu ya anthu.


Ngati thupi lonse likadakhala diso, kukadakhala kuti kununkhiza?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa