Masalimo 139:8 - Buku Lopatulika8 Ndikakwera kunka kumwamba, muli komweko; kapena ndikadziyalira ku Gehena, taonani, muli komweko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndikakwera kunka kumwamba, muli komweko; kapena ndikadziyalira ku Gehena, taonani, muli komweko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Ndikakwera kumwamba, Inu muli komweko, ndikagona m'dziko la anthu akufa, Inu muli momwemo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Ndikakwera kumwamba, Inu muli komweko; ndikakagona ku malo a anthu akufa, Inu muli komweko. Onani mutuwo |