Masalimo 139:6 - Buku Lopatulika6 Kudziwa ichi kundiposa ndi kundidabwitsa: Kundikhalira patali, sindifikirako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Kudziwa ichi kundilaka ndi kundidabwitsa: Kundikhalira patali, sindifikirako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Nzeru zimenezi nzopitirira nzeru zanga, nzapamwamba, sindingathe kuzimvetsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Nzeru zimenezi ndi zopitirira nzeru zanga, ndi zapamwamba kuti ine ndizipeze. Onani mutuwo |