Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 139:5 - Buku Lopatulika

5 Munandizinga kumbuyo ndi kumaso, nimunaika dzanja lanu pa ine.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Munandizinga kumbuyo ndi kumaso, nimunaika dzanja lanu pa ine.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Mumandizinga kumbuyo ndi kutsogolo, ndipo mumandisanjika dzanja lanu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Mumandizinga kumbuyo ndi kutsogolo komwe; mwasanjika dzanja lanu pa ine.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 139:5
6 Mawu Ofanana  

Palibe wakutiweruza, wakutisanjika ife tonse awiri manja ake.


Mngelo wa Yehova azinga kuwatchinjiriza iwo akuopa Iye, nawalanditsa iwo.


Koma sanatulutse dzanja lake pa akulu a ena a Israele; ndipo anapenya Mulungu, nadya, namwa.


Mulungu wamuyaya ndiye mokhaliramo mwako; ndi pansipo pali manja osatha. Ndipo aingitsa mdani pamaso pako, nati, Ononga.


Ndipo pamene ndinamuona Iye, ndinagwa pa mapazi ake ngati wakufa; ndipo anaika dzanja lake lamanja pa ine, nati, Usaope, Ine ndine Woyamba ndi Wotsiriza,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa