Masalimo 139:4 - Buku Lopatulika4 Pakuti asanafike mau pa lilime langa, taonani, Yehova, muwadziwa onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Pakuti asanafike mau pa lilime langa, taonani, Yehova, muwadziwa onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ngakhale mau anga asanafike pakamwa panga, Inu Chauta mumaŵadziŵa onse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Mawu asanatuluke pa lilime langa mumawadziwa bwinobwino, Inu Yehova. Onani mutuwo |