Masalimo 139:23 - Buku Lopatulika23 Mundisanthule, Mulungu, nimudziwe mtima wanga; mundiyese nimudziwe zolingalira zanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Mundisanthule, Mulungu, nimudziwe mtima wanga; mundiyese nimudziwe zolingalira zanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Fufuzeni, Inu Mulungu, kuti mudziŵe mtima wanga. Yeseni kuti mudziŵe maganizo anga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Santhuleni, Inu Mulungu ndipo mudziwe mtima wanga; Yeseni ndipo mudziwe zolingalira zanga. Onani mutuwo |