Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 139:22 - Buku Lopatulika

22 Ndidana nao ndi udani weniweni, ndiwayesa adani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Ndidana nao ndi udani weniweni, ndiwayesa adani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Ndimadana nawo ndi chidani chenicheni. Ndimaŵayesa adani anga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Ndimadana nawo kwathunthu; ndi adani anga.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 139:22
2 Mawu Ofanana  

Munthu akadza kwa Ine, wosada atate wake ndi amake, ndi mkazi wake, ndi ana, ndi abale, ndi alongo ake, inde ndi moyo wake womwe wa iye mwini, sangathe kukhala wophunzira wanga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa