Masalimo 139:18 - Buku Lopatulika18 Ndikaziwerenga zichuluka koposa mchenga: Ndikauka ndikhalanso nanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndikaziwerenga zichuluka koposa mchenga: Ndikauka ndikhalanso nanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Ndikadaŵaŵerenga, bwenzi ali ambiri koposa mchenga. Ndikamadzuka ndimakhala nanube. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ndikanaziwerenga, zikanakhala zochuluka kuposa mchenga; pamene ndadzuka, ndili nanube. Onani mutuwo |