Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 139:17 - Buku Lopatulika

17 Potero, Mulungu, ndiziyesa zolingalira zanu za mtengo wake ndithu! Mawerengedwe ake ndi ambirimbiri!

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Potero, Mulungu, ndiziyesa zolingalira zanu za mtengo wake ndithu! Mawerengedwe ake ndi ambirimbiri!

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Maganizo anu, Inu Mulungu, ndi ozama kwa ine, ndi osaŵerengeka konse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Zolingalira zanu pa ine ndi zamtengowapatali, Inu Mulungu, ndi zosawerengeka ndithu!

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 139:17
10 Mawu Ofanana  

Ndipo Isaki anatuluka kulingalira m'munda madzulo; ndipo anatukula maso ake, nayang'ana, taona, ngamira zinalinkudza.


Ha! Kukoma kwanu ndiko kwakukulu nanga, kumene munasungira iwo akuopa Inu, kumene munachitira iwo akukhulupirira Inu, pamaso pa ana a anthu!


Ha! Chifundo chanu, Mulungu, nchokondedwadi! Ndipo ana a anthu athawira kumthunzi wa mapiko anu.


Inu, Yehova, Mulungu wanga, zodabwitsa zanu mudazichita nzambiri, ndipo zolingirira zanu za pa ife; palibe wina wozifotokozera Inu; ndikazisimba ndi kuzitchula, zindichulukira kuziwerenga.


Nsembe ndi chopereka simukondwera nazo; mwanditsegula makutu. Nsembe yopsereza ndi yamachimo simunapemphe.


Ha! Ntchito zanu nzazikulu, Yehova, zolingalira zanu nzozama ndithu.


ndi kukondwera ndi dziko lake lokhalamo anthu, ndi kusekerera ndi ana a anthu.


Pakuti ndidziwa malingiriro amene ndilingiririra inu, ati Yehova, malingiriro a mtendere, si a choipa, akukupatsani inu adzukulu ndi chiyembekezero.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa