Masalimo 136:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo anawapha mafumu omveka; pakuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo anawapha mafumu omveka; pakuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Adaphanso mafumu otchuka, pakuti chikondi chake nchamuyaya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Napha mafumu amphamvu, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya. Onani mutuwo |