Masalimo 136:17 - Buku Lopatulika17 Amene anapanda mafumu aakulu; pakuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Amene anapanda mafumu akulu; pakuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Adapha mafumu amphamvu, pakuti chikondi chake nchamuyaya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Amene anakantha mafumu akuluakulu, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya. Onani mutuwo |